Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 9/14 tsamba 3
  • Ndandanda ya Mlungu wa September 22

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa September 22
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA SEPTEMBER 22
Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
km 9/14 tsamba 3

Ndandanda ya Mlungu wa September 22

MLUNGU WOYAMBIRA SEPTEMBER 22

Nyimbo Na. 34 ndi Pemphero

Phunziro la Baibulo la Mpingo:

cl mutu 1 ndime 18-23 (Mph. 30)

Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Numeri 30-32 (Mph. 10)

Na. 1: Numeri 32:16-30 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Kodi N’chifukwa Chiyani Mulungu Sanawononge Satana Mwamsanga Atangopanduka?—rs tsa. 354 ndime 2–tsa. 355 ndime 1 (Mph. 5)

Na. 3: N’chifukwa Chiyani Adamu Ndi Hava Sanamvere Yehova?—bh tsa. 61 ndime 9-11 (Mph. 5)

Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 93

Mph. 15: Utumiki wa Umishonale Umabweretsa Madalitso. (Miy. 10:22) Nkhani yokambirana yochokera mu Buku Lapachaka la 2014, tsamba 123 ndime 2 mpaka tsamba 127 ndime 4 komanso tsamba 169. Pemphani omvera kuti afotokoze zimene tikuphunzirapo.

Mph. 15: “Muzigwiritsa Ntchito Webusaiti Yathu ya jw.org/ny Polalikira.” Nkhani yokambirana. Chitani chitsanzo pogwiritsa ntchito chitsanzo chomwe chili m’ndime 2. Kenako funsani omvera mafunso awa: N’chifukwa chiyani kupanga dawunilodi vidiyoyi n’kukhala nayo pa foni kapena pa chipangizo china kuli kothandiza? N’chifukwa chiyani kuli kofunika kuti tizitsegula vidiyoyi n’kuonetsa munthu tisananene zambiri komanso tisanamupemphe ngati akufuna kuionera kapena ayi? Kodi ndi zinthu ziti zimene zinachitika pamene munkagwiritsa ntchito vidiyoyi mu utumiki? Pomaliza, pemphani ofalitsa kuti aidziwe bwino webusaiti yathu ya jw.org/ny komanso kuti azigwiritsa ntchito webusaitiyi polalikira. Popeza si onse amene ali ndi foni kapena zipangizo zina zokhala ndi Intaneti, sankhani kapepala kamodzi pa timapepala tatsopano ndipo chitani chitsanzo chosonyeza mmene tingatigawirire mu utumiki. Limbikitsani onse kuti azigwiritsa ntchito timapepalati akamalalikira.

Nyimbo Na. 84 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena