Ndandanda ya Mlungu wa April 13
MLUNGU WOYAMBIRA APRIL 13
Nyimbo Na. 21 ndi Pemphero
Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 11 ndime 9-16 (Mph. 30)
Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 1 Samueli 19-22 (Mph. 8)
Na. 1: 1 Samueli 21:10-15 ndi 22:1-4 (Osapitirira mph. 3)
Na. 2: Tizilimbikitsa Ndiponso Kutonthoza Anthu mu Utumiki—bt tsa. 85-86 ndime 3-4 ndi bokosi patsamba 86 (Mph. 5)
Na. 3: N’chifukwa Chiyani Anthufe Timavutika?—igw tsa. 15 ndime 1-4 (Mph. 5)
Msonkhano wa Utumiki:
Mutu wa Mwezi Uno: “Muzigwiritsa ntchito bwino nthawi yanu.”—Aef. 5:15, 16.
Mph. 10: “Muzigwiritsa Ntchito Bwino Nthawi Yanu.” Nkhani yofotokoza mutu wa mwezi uno.—Aef. 5:15, 16; onani Nsanja ya Olonda ya May 15, 2012, tsamba 19-20 ndime 11-14.
Mph. 20: “Muzigwiritsa Ntchito Bwino Nthawi Mukakhala mu Utumiki.” Nkhani yokambirana.
Nyimbo Na. 98 ndi Pemphero