Ndandanda ya Mlungu wa August 17
MLUNGU WOYAMBIRA AUGUST 17
Nyimbo Na. 1 ndi Pemphero
Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 17 ndime 9-16 (30 min.)
Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 2 Mafumu 1-4 (8 min.)
Na. 1: 2 Mafumu 1:11-18 (Osapitirira 3 min.)
Na. 2: Mavuto Amene Angabwere Chifukwa Chocheza ndi Anthu Olakwika—lv tsa. 102-105 ndime 13-17 (5 min.)
Na. 3: Zimene Tiyenera Kuchita Kuti Tikhale pa Ubwenzi ndi Mulungu—igw tsa. 28 ndime 5–tsa. 29 ndime 3 (5 min.)
Msonkhano wa Utumiki:
Mutu wa Mwezi Uno: “Ine ndi a m’nyumba yanga, tizitumikira Yehova.”—Yos. 24:15.
30 min: “Mawu Awa . . . Azikhala Pamtima Pako.” Mafunso ndi mayankho. Kambiranani mafunso omwe ali m’nkhaniyi. Gwiritsani ntchito mfundo za m’ndime yoyamba monga mawu oyamba ndipo mugwiritse ntchito mfundo za m’ndime yomaliza monga mawu omaliza. Ngati abale ambiri a mumpingo mwanu sangathe kuonera vidiyoyi kunyumba kwawo, kambiranani funso 3, 4, 5, 7, 9, 10 ndi 15.
Nyimbo Na. 88 ndi Pemphero