Ndandanda ya Mlungu wa November 23
MLUNGU WOYAMBIRA NOVEMBER 23
Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero
Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 22 ndime 1-8 (30 min.)
Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 2 Mbiri 1-5 (8 min.)
Na. 1: 2 Mbiri 3:14-17 mpaka 4:1-6 (Osapitirira 3 min.)
Na. 2: Yendani ndi Yehova—ia tsa. 17-19 ndime 4-8 (5 min.)
Na. 3: Kodi Kubatizidwa N’kofunika Bwanji kwa Akhristu?—bh tsa. 174-175 ndime 1-4 (5 min.)
Msonkhano wa Utumiki:
Mutu wa Mwezu Uno: “Ineyo ndinabzala, Apolo anathirira, koma Mulungu ndiye anakulitsa.”—1 Akor. 3:6.
10 min: “Kukonzekera Bwino N’kofunika Kuti Tiziphunzitsa Mwaluso.” Nkhani.
10 min: Makhalidwe Abwino Amathandiza Kuti Anthu Azimvetsera Uthenga Wathu. Nkhani yokambirana yochokera mu Buku Lapachaka la 2015 tsamba 49, ndime 3, mpaka tsamba 52, ndime 1; ndiponso tsamba 140, ndime 3, mpaka tsamba 141, ndime 3. Pemphani omvera kuti afotokoze zimene akuphunzirapo.
10 min: “Muzigwiritsa Ntchito Bwino Buku Lakuti Baibulo Limaphunzitsa Chiyani.” Nkhani yokambirana. Chitani chitsanzo chachidule.
Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero