Zilengezo
◼ Mabuku ogawira mu November ndi December: Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? kapena timapepala totsatirati: Kodi Baibulo Mumalikhulupirira?, Kodi Dziko Lapansili Lili M’manja mwa Ndani?, Kodi Mavuto Amene Tikukumana Nawowa Adzathadi?, Kodi Mukuganiza Kuti Zinthu Zidzakhala Bwanji M’tsogolo?, Kodi N’chiyani Chingathandize Kuti Banja Likhale Losangalala?, Kodi N’zoonadi Kuti Akufa Adzauka? ndiponso Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani? January ndi February 2016: Timabuku takuti, Mverani Mulungu, Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha kapena kakuti Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu.