Ndandanda ya Mlungu wa November 30
MLUNGU WOYAMBIRA NOVEMBER 30
Nyimbo Na. 57 ndi Pemphero
Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 22 ndime 9-17 (30 min.)
Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 2 Mbiri 6-9 (8 min.)
Na. 1: 2 Mbiri 6:22-27 (Osapitirira 3 min.)
Na. 2: N’chifukwa Chiyani Kumvera Mulungu si Kophweka Nthawi Zonse?—ia tsa. 27-28 ndime 8-13 (5 min.)
Na. 3: Kodi Achinyamata Angaphunzire Chiyani kwa Samueli?—ia tsa. 63 ndime 16-18 (5 min.)
Msonkhano wa Utumiki:
Mutu wa Mwezu Uno: “Ineyo ndinabzala, Apolo anathirira, koma Mulungu ndiye anakulitsa.”—1 Akor. 3:6.
10 min: Zimene Munganene Pogawira Magazini. Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuchita chitsanzo cha zimene tinganene pogawira magaziniwa pogwiritsa ntchito zitsanzo za ulaliki. Ndiyeno kambiranani zitsanzozo.
10 min: Zofunika pampingo.
10 min: Kodi Tinachita Zotani? Nkhani yokambirana. Pemphani omvera kuti afotokoze mmene anapindulira pogwiritsa ntchito malangizo a m’nkhani yakuti, “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Kugawira Buku Lakuti Baibulo Limaphunzitsa Chiyani” Kenako apempheni kuti afotokoze zinthu zosangalatsa zimene zinachitika.
Nyimbo yatsopano Na. 141 ndi Pemphero
Kumbukirani kuti, muyenera kuika nyimboyi kuti onse amvetsere kenako muibwerezenso kuti onse aimbe nawo. Ngati simungathe kuchita dawunilodi nyimboyi pa webusaiti yathu, mungaimbe nyimbo nambala 47.