CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 2 MBIRI 33-36
Yehova Amakhululukira Munthu Amene Walapa Kuchokera Pansi pa Mtima
Losindikizidwa
MANASE
Yehova analola kuti amangidwe ndi Asuri n’kupita ku Babulo
MU ULAMULIRO WAKE ASANAMANGIDWE
Anamanga maguwa ansembe a milungu yonyenga
Anapereka nsembe ana ake
Anapha anthu osalakwa
Analimbikitsa zamizimu m’dziko lonse
MU ULAMULIRO WAKE ATAMASULIDWA
Anadzichepetsa kwambiri
Anapemphera kwa Yehova n’kupereka nsembe
Anawononga maguwa ansembe a milungu yonyenga
Analimbikitsa Aisiraeli onse kuti azitumikira Yehova
YOSIYA
MU ULAMULIRO WAKE
Anafunafuna Yehova
Anayeretsa Yuda ndi Yerusalemu
Anakonza nyumba ya Yehova ndipo anapeza buku la Chilamulo