Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 May tsamba 5
  • May 16-22

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 16-22
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 May tsamba 5

May 16-22

MASALIMO 11-18

  • Nyimbo Na. 106 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Ndani Angakhale Mlendo M’chihema cha Yehova?”: (10 min.)

    • Sal. 15:1, 2—Tizilankhula zoona mumtima mwathu (w03 8/1 14 ndime 18; w89 9/15 27 ¶1)

    • Sal. 15:3—Tiyenera kulankhula zinthu zabwino (w89 10/15 12 ndime 10-11; w89 9/15 27 ndime 3-4; w14 2/15 23, ndime 10-11)

    • Sal. 15:4, 5—Tizikhala okhulupirika nthawi zonse (w06 5/15 19 ndime 1; w89 9/15 29-30; it-1-E 1211 ndime 3)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Sal. 11:3—Kodi vesili likutanthauza chiyani? (w06 5/15 18 ndime 2; w05 5/15 32 ndime 2)

    • Sal. 16:10—Kodi ulosiwu unakwaniritsidwa bwanji pa Yesu Khristu? (w11 8/15 16 ndime 19; w05 5/1 14 ndime 9)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 18:1-19

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp16.3 16—Werengani lemba pogwiritsa ntchito foni kapena chipangizo china chamakono.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp16.3 16—Tsegulani Laibulale ya JW ndi kuwerenga malemba n’cholinga choti mwininyumba amve malembawo m’chinenero chake.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 100-101 ndime 10-11—Sonyezani mwachidule wophunzirayo mmene angagwiritsire ntchito Laibulale ya JW pofufuza yankho la funso limene wafunsa.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 70

  • “Mmene Tingagwiritsire Ntchito Laibulale ya JW”—Gawo 1: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani mavidiyo akuti Ikani Kachizindikiro Kokuthandizani Kukumbukira ndi Onani Zimene Munatsegula, ndipo kambiranani mwachidule zomwe zili m’mavidiyowo. Kenako kambiranani mitu iwiri yoyambirira m’nkhaniyi. Pemphani abale ndi alongo kuti afotokoze mmene anagwiritsira ntchito Laibulale ya JW pophunzira Baibulo paokha ndiponso pamisonkhano yampingo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) cl mutu 30 ndime 10-18

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 43 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena