Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 October tsamba 6
  • October 24-30

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 24-30
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 October tsamba 6

October 24-30

MIYAMBO 17-21

  • Nyimbo Na. 76 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yesetsani Kukhala Mwamtendere ndi Ena”: (10 min.)

    • Miy. 19:11—Muzikhala odekha munthu wina akakukhumudwitsani (w14 12/1 12-13)

    • Miy. 18:13, 17; 21:13—Muzitsimikizira kuti mukudziwa nkhani yonse (w11 8/15 30 ndime 11-14)

    • Miy. 17:9—Muzisonyeza chikondi pokhululukira munthu amene wakulakwirani (w11 8/15 31 ndime 17)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Miy. 17:5—Fotokozani chifukwa chimodzi chimene tiyenera kusankhira zosangalatsa mwanzeru. (w10 11/15 6 ndime 17; w10 11/15 31 ndime 15)

    • Miy. 20:25—Kodi mfundo ya pa lembali ingathandize bwanji anthu amene akufuna kukhala pa chibwenzi komanso kulowa m’banja? (w09 5/15 15-16 ndime 12-13)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Miy. 18:14-24; 19:1-10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) M’patseni munthuyo kapepala koitanira anthu kumisonkhano. (inv)

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) inv—Pomaliza, muuzeni kuti mukufuna kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 57 ndime 14-15—Thandizani munthuyo kuona kuti ayenera kusintha mmene amavalira akamapita kumisonkhano.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 77

  • Kukhazikitsa Mtendere Kumabweretsa Madalitso: (15 min.) Nkhani yokambirana. Poyamba, onetsani vidiyo yakuti Kukhazikitsa Mtendere Kumabweretsa Madalitso. Kenako funsani mafunso awa: Kodi tiyenera kupewa zinthu ziti tikasemphana maganizo ndi munthu wina? Kodi timapeza madalitso ati tikamatsatira mfundo za pa Miyambo 17:9 ndi Mateyu 5:23, 24?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 9 ndime 14-24 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 82.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 144 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena