Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 December tsamba 6
  • December 19-25

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 19-25
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 December tsamba 6

December 19-25

YESAYA 11-16

  • Nyimbo Na. 143 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Dziko Lapansi Lidzadzaza ndi Anthu Odziwa Yehova”: (10 min.)

    • Yes. 11:3-5—Chilungamo chidzakhalapo mpaka kalekale (ip-1 160-161 ¶9-11)

    • Yes. 11:6-8—Anthu azidzakhala mwamtendere ndi zinyama (w12 9/15 9-10 ¶8-9)

    • Yes. 11:9—Anthu onse adzaphunzira zimene Yehova amafuna (w16.06 8 ¶9; w13 6/1 7)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yes. 11:1, 10—Kodi Yesu Khristu angakhale bwanji nthambi yotuluka “pachitsa cha Jese” ndiponso “muzu wa Jese”? (w06 12/1 9 ¶6)

    • Yes. 13:17—N’chifukwa chiyani Baibulo limanena kuti Amedi ankaona kuti siliva si kanthu komanso sankasangalala ndi golide? (w06 12/1 10 ¶10)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 13:17-22; 14:1-8

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yobu 34:10—Kuphunzitsa Choonadi.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Mlal. 8:9; 1 Yoh. 5:19—Kuphunzitsa Choonadi.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 54 ¶9—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 24

  • “Zimene Mulungu Amatiphunzitsa Zimatithandiza Kuti Tisakhale Atsankho”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti, Johny ndi Gideon: Anali Khoswe ndi Mphaka Koma Pano Ndi Ogwirizana.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 13 ¶13-25 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 114

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 151 ndi Pemphero

    Kumbukirani: Muyenera kuika nyimboyi kuti onse amvetsere, kenako muibwerezenso kuti onse aimbe nawo.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena