December Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano December 2016 Zitsanzo za Ulaliki December 5-11 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 1-5 “Tiyeni Tipite Kukakwera Phiri la Yehova” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Tizifika Anthu Pamtima ndi Buku Lakuti Kodi Mungatani Kuti ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’? December 12-18 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 6-10 Mesiya Anakwaniritsa Ulosi MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Ine Ndilipo! Nditumizeni” December 19-25 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 11-16 Dziko Lapansi Lidzadzaza ndi Anthu Odziwa Yehova MOYO WATHU WACHIKHRISTU Zimene Mulungu Amatiphunzitsa Zimatithandiza Kuti Tisakhale Atsankho December 26–January 1 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 17-23 Munthu Akamagwiritsa Ntchito Udindo Wake Molakwika Amachotsedwa pa Udindowo