Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 December tsamba 4
  • December 12-18

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 12-18
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 December tsamba 4

December 12-18

YESAYA 6-10

  • Nyimbo Na. 116 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mesiya Anakwaniritsa Ulosi”: (10 min.)

    • Yes. 9:1, 2—Malemba ananeneratu kuti adzagwira ntchito yolalikira ku Galileya (w11 8/15 10 ¶13; ip-1 124-126 ¶13-17)

    • Yes. 9:6—Adzakhala ndi maudindo ambiri (w14 2/15 12 ¶18; w07 5/15 6)

    • Yes. 9:7—Ulamuliro wake udzabweretsa mtendere weniweni ndiponso chilungamo (ip-1 132 ¶28-29)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yes. 7:3, 4—N’chifukwa chiyani Yehova anapulumutsa Ahazi yemwe anali mfumu yoipa? (w06 12/1 9 ¶4)

    • Yes. 8:1-4—Kodi ulosi umenewu unakwaniritsidwa bwanji? (it-1-E 1219; ip-1 112 ¶23-24)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  •   Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 7:1-17

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g16.6 chikuto

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g16.6 chikuto

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 34 ¶18—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 10

  • “Ine Ndilipo! Nditumizeni” (Yes. 6:8): (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Kusamukira Kumene Kukufunika Olalikira Ambiri.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 13 ¶1-12.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 150 ndi Pemphero

    Kumbukirani: Muyenera kuika nyimboyi kuti onse amvetsere, kenako muibwerezenso kuti onse aimbe nawo.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena