Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 January tsamba 7
  • January 30–February 5

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 30–February 5
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 January tsamba 7

January 30–February 5

YESAYA 43-46

  • Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Ndi Mulungu Yemwe Amalosera Zoona”: (10 min.)

    • Yes. 44:26-28—Yehova analosera kuti Yerusalemu ndiponso kachisi adzamangidwanso komanso kuti Koresi ndi amene adzagonjetse Babulo (ip-2 71-72 ¶22-23)

    • Yes. 45:1, 2—Yehova ananeneratu mmene Babulo adzagonjetsedwere (ip-2 77-78 ¶4-6)

    • Yes. 45:3-6—Yehova anafotokoza chifukwa chake anagwiritsa ntchito Koresi kuti agonjetse Babulo (ip-2 79-80 ¶8-10)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yes. 43:10-12—Kodi Aisiraeli anayenera kuchita chiyani kuti akhale mboni za Yehova? (w14 11/15 21-22 ¶14-16)

    • Yes. 43:25—Kodi chifukwa chachikulu chimene Yehova amafafanizira zolakwa zathu n’chiyani? (ip-2 60 ¶24)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 46:1-13

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) kt—Kulalikira mnzanu wakusukulu kapena wakuntchito.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) kt—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) jl mutu 4

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 143

  • Kodi Tingadziwe Bwanji Kuti Baibulo Limanena Zoona?: (15 min.) Onetsani vidiyo yakuti Kodi Tingadziwe Bwanji Kuti Baibulo Limanena Zoona? Kenako kambiranani mafunso awa: Kodi tingagwiritse ntchito bwanji vidiyoyi tikamalalikira mwamwayi, pamalo opezeka anthu ambiri komanso kunyumba ndi nyumba? Kodi ndi zinthu zosangalatsa ziti zimene mwakumana nazo pogwiritsa ntchito vidiyoyi?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 16 ¶16-29, bokosi patsamba 142 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 144.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena