CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 43-46
Yehova Ndi Mulungu Yemwe Amalosera Zoona
Losindikizidwa
Kutatsala zaka pafupifupi 200 kuti mzinda wa Babulo uwonongedwe, Yehova ananeneratu mwatsatanetsatane kudzera mwa Yesaya zimene zidzachitike pogonjetsa mzindawo.
Koresi ndi amene adzagonjetse Babulo
Zitseko za mzindawo zidzakhala zotsegula
Mtsinje wa Firate, womwe unkateteza mzindawu, ‘udzaumitsidwa’