Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 March tsamba 3
  • March 13-19

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 13-19
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 March tsamba 3

March 13-19

YEREMIYA 5-7

  • Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Anasiya Kuchita Zimene Mulungu Ankafuna”: (10 min.)

    • Yer. 6:13-15​—Yeremiya anaulula machimo a Aisiraeli (w11 3/15 29 ¶4; w88 4/1 11-12 ¶7-8)

    • Yer 7:1-7​—Yehova anayesetsa kuwathandiza kuti alape (w88 4/1 12 ¶9-10; jr 70 ¶8)

    • Yer 7:8-15​—Aisiraeli ankaganiza kuti Yehova sangachite chilichonse (jr 21 ¶12)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yer 6:16​—Kodi Yehova ankalangiza anthu ake kuti achite chiyani? (w05 11/1 23 ¶11)

    • Yer 6:22, 23​—N’chifukwa chiyani Yeremiya ananena kuti “anthu akubwera kuchokera kudziko la kumpoto”? (w88 4/1 13 ¶15)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 5:26-31; 6:1-5

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.)T-36 Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) T-36 Kambiranani“mbali yakuti “Ganizirani Mfundo Iyi.” Muitanireni ku Chikumbutso.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) jl mutu 1—Muitanireni ku Chikumbutso.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 125

  • “Kodi Tingagwiritse Ntchito Bwanji Kabuku Kakuti Kodi Ndani Akuchita Chifuniro cha Yehova Masiku Ano?”: (15 min.) Yambani ndi kukambirana nkhaniyi kwa maminitsi 5. Kenako onetsani ndiponso kukambirana vidiyo imene ikusonyeza mmene tingaphunzirire ndi munthu mutu 8 wa m’kabukuka. Limbikitsani onse amene ali ndi maphunziro a Baibulo kuti azigwiritsa ntchito kabukuka mlungu uliwonse.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 19 ¶17-31, bokosi patsamba 170 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 171

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 10 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena