CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 1-4
“Ine Ndili ndi Iwe Kuti Ndikulanditse”
Losindikizidwa
N’kutheka kuti Yeremiya anali ndi zaka pafupifupi 25 pamene Yehova anamuika kukhala mneneri. Yeremiya ankaona kuti sangakwanitse ntchito imeneyi, koma Yehova anamutsimikizira kuti amuthandiza.
647
Yeremiya anaikidwa kukhala mneneri
607
Yerusalemu anawonongedwa
580
Nthawi imene anamaliza kulemba bukuli
Zaka zonsezi ndi za B.C.E.