Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 March tsamba 2
  • March 6-12

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 6-12
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 March tsamba 2

March 6-12

YEREMIYA 1-4

  • Nyimbo Na. 23 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Ine Ndili ndi Iwe Kuti Ndikulanditse”: (10 min.)

    • [Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yeremiya.]

    • Yer. 1:6​—Yeremiya ankakayikira kuti angakwanitse ntchito imene anapatsidwa (w11 3/15 29 ¶4)

    • Yer. 1:7-10, 17-19—Yehova analonjeza kuti amulimbikitsa ndiponso kumuthandiza (w05 12/15 24 ¶18; jr 88 ¶14-15)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yer. 2:13, 18​—Kodi Aisiraeli osakhulupirika anachita zinthu ziwiri ziti zomwe zinali zoipa? (w07 3/15 9 ¶8)

    • Yer. 4:10​—Kodi mawu oti Yehova ‘anapusitsa’ anthu ake akutanthauza chiyani? (w07 3/15 9 ¶4)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 4:1-10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Kukambirana Zitsanzo za Ulaliki. Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 149

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya March.

  • Ntchito Yoitanira Anthu ku Chikumbutso Idzayamba pa 18 March: (8 min.) Nkhani yokambidwa ndi woyang’anira utumiki yochokera mu Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya February 2016, tsamba 8. Perekani kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso kwa aliyense n’kukambirana mfundo zake. Fotokozani zimene mpingo wakonza pofuna kuti mudzathe kugawira timapepalati kwa anthu onse a m’gawo lanu.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 19 ¶1-16

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 74 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena