June 26–July 2
Ezekieli 6-10
Nyimbo Na. 141 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mudzalembedwa Chizindikiro Choti Ndinu Woyenera Kupulumuka?”: (10 min.)
Ezek. 9:1, 2—Masomphenya amene Ezekieli anaona ndi othandizanso kwa ife (w16.06 16-17)
Ezek. 9:3, 4—Pa nthawi ya chisautso chachikulu, anthu amene amamvetsera tikamawalalikira adzalembedwa chizindikiro choti ndi oyenera kupulumuka
Ezek. 9:5-7—Yehova sadzawononga anthu olungama pamodzi ndi oipa
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Ezek. 7:19—Kodi vesi limeneli lingatithandize bwanji kukonzekera zam’tsogolo? (w09 9/15 23 ¶10)
Ezek. 8:12—Kodi vesili likusonyeza bwanji kuti munthu amene alibe chikhulupiriro n’zosavuta kuti achite zoipa? (w11 4/15 26 ¶14)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 8:1-12
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Chiv. 4:11—Kuphunzitsa Choonadi.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Sal. 11:5; 2 Akor. 7:1—Kuphunzitsa Choonadi.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 127 ¶4-5—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Tizitsatira Mfundo za Makhalidwe Abwino za Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Khalani Bwenzi La Yehova—Mwamuna Mmodzi, Mkazi Mmodzi (imapezeka pamene palembedwa kuti ANA).
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 2 ¶35-40, komanso tsamba 25, 26-27, 28-29
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero