July 24-30
EZEKIELI 21-23
Nyimbo Na. 99 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Ufumu Unaperekedwa kwa Amene Ndi Woyenerera Mwalamulo”: (10 min.)
Ezek. 21:25—“Mtsogoleri wa Isiraeli woipa” anali Mfumu Zedekiya (w07 7/1 13 ¶11)
Ezek. 21:26—Anthu a m’banja la Davide omwe ankalamulira ali ku Yerusalemu anasiya kukhala mafumu (w11 8/15 9 ¶6)
Ezek. 21:27—Yesu Khristu ndi amene ali “woyenerera mwalamulo” kukhala Mfumu (w14 10/15 10 ¶14)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Ezek. 21:3—Kodi “lupanga” limene Yehova anasolola m’chimake ndi chiyani makamaka? (w07 7/1 14 ¶1)
Ezek. 23:49—Kodi chaputala 23 chikusonyeza kuti Aisiraeli ndi Ayuda anachita tchimo lotani, nanga ifeyo tikuphunzirapo chiyani? (w07 7/1 14 ¶6)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 21:1-13
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) fg—Mufotokozereni za vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (Koma musaonetse vidiyoyi).
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) bhs—Mufotokozereni munthu amene mumam’patsa magazini mwezi uliwonse za vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (Koma musaonetse vidiyoyi).
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 217 ¶1-3
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Tizisonyeza Ulemu Tikafika Pakhomo”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Ikambidwe ndi woyang’anira utumiki. Yambani ndi kuonetsa vidiyo yofotokoza zimene tingachite kuti tizisonyeza ulemu tikafika pakhomo la munthu.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 4 ¶7-15 komanso tsamba 44, 46
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero