CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 21-23
Ufumu Unaperekedwa kwa Amene Ndi Woyenerera Mwalamulo
Losindikizidwa
Pokwaniritsa ulosi wa Ezekieli, Yesu ndi amene anali “woyenerera mwalamulo” kukhala mfumu.
Kodi Mesiya anabadwira mu mtundu uti?
Kodi ndi ufumu uti umene Yehova ananena kuti udzakhazikika mpaka kalekale
Kodi Mateyu anati Yesu anali wa mu mzera wobadwira chifukwa cha kholo liti?