July Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya July 2017 Zitsanzo za Ulaliki July 3-9 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 11-14 Kodi Muli ndi Mtima Wofewa Ngati Mnofu? July 10-16 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 15-17 Kodi Mumakwaniritsa Zimene Mwalonjeza? July 17-23 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 18-20 Kodi Yehova Akatikhululukira Machimo, Amawakumbukirabe? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mumadziimbabe Mlandu Yehova Akakukhululukirani? July 24-30 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 21-23 Ufumu Unaperekedwa kwa Amene Ndi Woyenerera Mwalamulo MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tizisonyeza Ulemu Tikafika Pakhomo July 31–August 6 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 24-27 Ulosi Wonena za Kuwonongedwa kwa Turo Umatithandiza Kuti Tizikhulupirira Kwambiri Mawu a Yehova