August 14-20
EZEKIELI 32-34
Nyimbo Na. 144 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Udindo Waukulu wa Mlonda”: (10 min.)
Ezek. 33:7—Yehova anaika Ezekieli kukhala mlonda (it-2 1172 ¶2)
Ezek. 33:8, 9—Mlonda akachenjeza anthu ankapewa mlandu wamagazi (w88 1/1 28 ¶13)
Ezek. 33:11, 14-16—Yehova adzapulumutsa anthu amene amamvera akachenjezedwa (w12 3/15 15 ¶3)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Ezek. 33:32, 33—N’chifukwa chiyani tiyenera kupitirizabe kulalikira ngakhale kuti anthu ena amatitsutsa kapena kutinyoza? (w91 3/15 17 ¶16-17)
Ezek. 34:23—Kodi vesi limeneli likukwaniritsidwa bwanji? (w07 4/1 26 ¶3)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 32:1-16
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.4 chikuto—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.4 chikuto—Muitanireni kumisonkhano.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 2 ¶9-10—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzikhala ndi Makhalidwe Amene Mulungu Amasangalala Nawo—Kulimba Mtima”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Muzipewa Zinthu Zimene Zingawononge Khalidwe Lanu la Kukhulupirika—Kuopa Anthu.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 5 ¶10-17 komanso tsamba 53
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 117 ndi Pemphero