October 9-15
DANIELI 10-12
Nyimbo Na. 31 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Ananeneratu Zokhudza Mafumu a Mtsogolo”: (10 min.)
Dan. 11:2—Mafumu 4 analamulira mu ufumu wa Perisiya (dp 212-213 ¶5-6)
Dan. 11:4—Ufumu wa Alekizanda unagawanika n’kukhala maufumu 4 (dp 214 ¶11)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Dan. 12:3—Kodi “anthu ozindikira” ndi ndani, nanga ndi liti pamene “adzawala ngati kuwala kwa kuthambo”? (w13 7/15 13 ¶16, mawu akumapeto)
Dan. 12:13—Kodi Yehova anamulonjeza chiyani Danieli? (dp 315 ¶18)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Dan. 11:28-39
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.5 chikuto—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.5 chikuto—Pitirizani kukambirana zokhudza magazini imene munamupatsa kale. Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.
Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w16.11 5-6 ¶7-8—Mutu: Kodi Tingatsanzire Bwanji Chitsanzo cha Yehova pa Nkhani Yolimbikitsa Ena?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Timalimbikitsidwa ndi Maulosi a M’Baibulo: (15 min.) Onetsani vidiyo yakuti ‘Mawu a Ulosi’ Amatilimbikitsa.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 8 ¶8-13, komanso tsamba 83
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero