Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 February tsamba 2
  • February 5-11

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 5-11
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 February tsamba 2

February 5-11

MATEYU 12-13

  • Nyimbo Na. 27 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Fanizo la Tirigu ndi Namsongole”: (10 min.)

    • Mat. 13:24-26​—Munthu anafesa mbewu zabwino m’munda mwake, koma mdani wake anabwera n’kudzafesamo namsongole (w13 7/15 9-10 ¶2-3)

    • Mat. 13:27-29​—Tirigu ndi namsongole zinakulira pamodzi mpaka nthawi yokolola (w13 7/15 10 ¶4)

    • Mat. 13:30​—Nthawi yokolola itafika, okolola anasonkhanitsa namsongole kenako anasonkhanitsa tirigu (w13 7/15 12 ¶10-12)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Mat. 12:20​—Kodi tingatsanzire bwanji khalidwe la Yesu lochitira ena chifundo? (“nyale yofuka” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 12:20, nwtsty)

    • Mat. 13:25​—Kodi zinkachitikadi kuti munthu ankafesa namsongole m’munda umene mnzake wafesamo tirigu? (w16.10 32)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 12:1-21

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 22-23 ¶10-12

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 68

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • “Mfundo Zimene Tingaphunzire Kuchokera M’mafanizo Onena za Ufumu”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Kambiranani mmene mafanizo amenewa angatithandizire kuti tizichita khama polalikira.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 13 ¶33-34 ndi bokosi patsamba “145 komanso tsamba 146-147

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 10 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena