February Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya February 2018 Zimene Tinganene February 5-11 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 12-13 Fanizo la Tirigu ndi Namsongole MOYO WATHU WACHIKHRISTU Mfundo Zimene Tingaphunzire Kuchokera M’mafanizo Onena za Ufumu February 12-18 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 14-15 Yesu Amadyetsa Anthu Ambiri Kudzera Mwa Anthu Ochepa MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Uzilemekeza Bambo Ako ndi Mayi Ako” February 19-25 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 16-17 Kodi Mumayendera Maganizo a Ndani? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kuwonjezera Luso Lathu Mu Utumiki—Muzigwiritsa Ntchito Mafunso Mwaluso February 26–March 4 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 18-19 Tizipewa Kuchita Zinthu Zimene Zingakhumudwitse Ena