Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 February tsamba 5
  • Yesu Amadyetsa Anthu Ambiri Kudzera Mwa Anthu Ochepa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yesu Amadyetsa Anthu Ambiri Kudzera Mwa Anthu Ochepa
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Yesu Amadyetsa Anthu Ambiri Kudzera mwa Anthu Ochepa
    Nsanja ya Olonda—2013
  • “Ndani Kwenikweni Amene Ali Kapolo Wokhulupirika ndi Wanzeru?”
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Anadyetsa Anthu Masauzande Ambiri ndi Mikate Komanso Nsomba Zochepa
    Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo
  • “Kumbukirani Amene Akutsogolera Pakati Panu”
    Gulu Lochita Chifuniro cha Mulungu
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 February tsamba 5
Ophunzira a Yesu akudyetsa khamu la anthu

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 14-15

Yesu Amadyetsa Anthu Ambiri Kudzera Mwa Anthu Ochepa

Pasika wa mu 32 C.E. atayandikira, Yesu anachita chozizwitsa chimene chinalembedwa ndi anthu onse 4, omwe analemba mabuku a Uthenga Wabwino.

Yesu anakhazikitsa njira imene akuigwiritsabe ntchito masiku ano, yomwe ndi yofanana ndi zimene anachita pa nthawi ya chozizwitsachi.

14:16-21

  • Yesu anauza ophunzira ake kuti adyetse khamu la anthu ngakhale kuti anali ndi mikate 5 komanso nsomba ziwiri zokha

  • Yesu anatenga mitanda ya mkate ndi nsomba zija ndipo atapemphera, anapatsa ophunzira ake omwe anagawira khamu la anthulo

  • Mozizwitsa, chakudyacho chinakwanira moti anthu onse anadya n’kukhuta. Yesu anadyetsa anthu ambiri kudzera mwa ophunzira ake omwe anali ochepa

    Yesu akugawa mkate kwa ophunzira ake; magazini ya Nsanja ya Olonda
  • Yesu ananeneratu kuti m’masiku otsiriza adzakhazikitsa njira yoperekera “chakudya pa nthawi yoyenera.”​—Mat. 24:45

  • Mu 1919, Yesu anasankha “kapolo wokhulupirika ndi wanzeru” yemwe ndi kagulu ka Akhristu odzozedwa, kuti aziyang’anira “antchito ake apakhomo” omwe ndi anthu odyetsedwa

  • Pogwiritsa ntchito kagulu ka Akhristu odzozedwawa, Yesu akutsatira njira yofanana ndi imene anagwiritsa ntchito m’nthawi ya atumwi

Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimazindikira komanso kulemekeza njira imene Yesu akugwiritsa ntchito podyetsa anthu?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena