Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 February tsamba 6
  • February 19-25

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 19-25
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 February tsamba 6

February 19-25

MATEYU 16-17

  • Nyimbo Na. 45 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mumayendera Maganizo a Ndani?”: (10 min.)

    • Mat. 16:21, 22​—Petulo analola kuti kutengeka maganizo kuzilamulira kaganizidwe kake (w07 2/15 16 ¶17)

    • Mat. 16:23​—Petulo anasiya kuyendera maganizo a Mulungu (w15 5/15 13 ¶16-17)

    • Mat. 16:24​—Akhristu ayenera kumayendera maganizo a Mulungu (w06 4/1 23 ¶9)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Mat. 16:18​—Kodi ndi ndani amene anali thanthwe lomwe Yesu anamangapo mpingo wachikhristu? (“Iwe ndiwe Petulo, ndipo pathanthwe ili” “mpingo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 16:18, nwtsty)

    • Mat. 16:19​—Kodi “makiyi a Ufumu wakumwamba” amene Yesu anapatsa Petulo anali chiyani? (“makiyi a Ufumu wakumwamba” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 16:19, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 16:1-20

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 78

  • “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Muzigwiritsa Ntchito Mafunso Mwaluso”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzigwira Ntchito Imene Yesu Anagwira​—Muziphunzitsa.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 14 ¶8-14 komanso bokosi patsamba 150

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena