Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 October tsamba 4
  • October 15-21

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 15-21
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 October tsamba 4

October 15-21

YOHANE 13-14

  • Nyimbo Na. 100 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Ndakupatsani Chitsanzo”: (10 min.)

    • Yoh. 13:5​—Yesu anasambitsa mapazi a ophunzira ake (“kusambitsa mapazi a ophunzira” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 13:5, nwtsty)

    • Yoh. 13:12-14​—Ophunzirawo ankayenera “kusambitsana mapazi” (“muyenera” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 13:14, nwtsty)

    • Yoh. 13:15​—Otsatira onse a Yesu ayenera kutengera chitsanzo chake pa nkhani ya kudzichepetsa (w99 3/1 31 ¶1)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yoh. 14:6​—Kodi Yesu ndi “njira, choonadi ndi moyo” m’njira yotani? (“Ine ndine njira, choonadi ndi moyo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 14:6, nwtsty)

    • Yoh. 14:12​—Kodi anthu amene amakhulupirira Yesu amachita bwanji “ntchito zazikulu” kuposa zimene iye anachita? (“ntchito zazikulu kuposa zimenezi” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 14:12, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 13:1-17

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Sonyezani mmene mungalalikirire mwamwayi pogwiritsa ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 114

  • “Akhristu Oona Amadziwika Chifukwa cha Chikondi​—Musamakhale ndi Mtima Wofuna Kuchita Zofuna Zanu Zokha Komanso Musamakwiye”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti ‘Muzikondana’​—Musamakhale ndi Mtima Wofuna Kuchita Zofuna Zanu Zokha Komanso Musamakwiye. Ngati nthawi ilipo kambiranani mfundo za m’kabokosi kakuti “Chitsanzo cha M’Baibulo Chofunika Kuchiganizira.”

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 9

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena