Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 March tsamba 3
  • March 11-17

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 11-17
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 March tsamba 3

March 11-17

AROMA 15-16

  • Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzidalira Yehova Kuti Akulimbikitseni Komanso Kukuthandizani Kupirira”: (10 min.)

    • Aroma 15:4​—Muziwerenga Mawu a Mulungu kuti azikulimbikitsani (w17.07 14 ¶11)

    • Aroma 15:5​—Muzipempha Yehova kuti akuthandizeni kukhala opirira komanso kuti akutonthozeni (w16.04 14 ¶5)

    • Aroma 15:13​—Yehova amatipatsa chiyembekezo (w14 6/15 14 ¶11)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Aroma 15:27​—Kodi anthu a mitundu ina omwe anadzakhala Akhristu “anali ndi ngongole” kwa Akhristu a ku Yerusalemu m’njira yotani? (w89 12/1 24 ¶3)

    • Aroma 16:25​—Kodi “chinsinsi chopatulika chimene chakhala chobisika kuyambira nthawi zakale” n’chiyani? (it-1 858 ¶5)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aroma 15:1-16 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 3)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri. (th phunziro 10)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri. (th phunziro 11)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 129

  • Yehova ‘Amatonthoza Komanso Amapereka Mphamvu’: (15 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa:

    • Kodi Yehova amatilimbikitsa bwanji?

    • Kodi mwaphunzira zotani pa nkhani yolimbikitsa ena?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 29

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 146 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena