May 13-19
2 Akorinto 7-10
Nyimbo Na. 109 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Utumiki Wothandiza Anthu pa Nthawi ya Mavuto”: (10 min.)
2 Akor. 8:1-3—Akhristu a ku Makedoniya anachita “zoposa” zimene akanatha pothandiza abale awo a ku Yudeya (w98 11/1 25 ¶1; kr 209 ¶1)
2 Akor. 8:4—Tikamathandiza Akhristu omwe akuvutika timakhala tikuchita “utumiki wothandiza” anthu (kr 209-210 ¶4-6)
2 Akor. 9:7—“Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera” (kr 196 ¶10)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
2 Akor. 9:15—Kodi ‘mphatso ya Mulungu yaulere imene sitingathe kuifotokoza’ n’chiyani? (w16.01 12 ¶2)
2 Akor. 10:17—Kodi ‘kudzitamanda mwa Yehova’ kumatanthauza chiyani? (g99 7/8 27)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 2 Akor. 7:1-12 (th phunziro 12)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri. (th phunziro 2)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri. (th phunziro 4)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Mmene Utumiki Wothandiza Anthu pa Nthawi ya Mavuto Wathandizira Akhristu a ku Caribbean”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Chikondi Chimaonekera ndi Zochita—Ntchito Yothandiza Anthu pa Zilumba za Caribbean.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 35 ¶28-36
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 89 ndi Pemphero