July 22-28
1 TIMOTEYO 1-3
Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yesetsani Kuti Mukhale Oyang’anira”: (10 min.)
[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 1 Timoteyo.]
1 Tim. 3:1—Abale onse akulimbikitsidwa kuti aziyesetsa kuti akhale oyang’anira mumpingo (w16.08 21 ¶3)
1 Tim. 3:13—Abale amene amatumikira bwino amalandira madalitso ambiri (km 9/78 4 ¶7)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
1 Tim. 1:4—N’chifukwa chiyani Paulo anachenjeza Timoteyo kuti asamataye nthawi kukambirana ndi anthu nkhani zokhudza mibadwo ya makolo? (it-1 914-915)
1 Tim. 1:17—N’chifukwa chiyani Yehova yekha ndi amene ayenera kutchedwa “Mfumu yamuyaya”? (cl 12 ¶15)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 1 Tim. 2:1-15 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 2)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) lvs 47-48 ¶6-7 (th phunziro 6)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Achinyamata Analemekeza Yehova ku Warwick: (6 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa:
Kodi abale ndi alongo achinyamata anathandiza bwanji ntchito yomanga ku Warwick, nanga anapindula bwanji?
Kodi abale ndi alongo achinyamata angalemekeze bwanji Yehova mumpingo?
“Mungaphunzire Zambiri Kuchokera kwa Achikulire”: (9 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Muzilemekeza Abale Achikulire.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 43 ndime 19-29
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 67 ndi Pemphero