July 29–August 4
1 TIMOTEYO 4-6
Nyimbo Na. 80 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kukhala Wodzipereka kwa Mulungu N’kofunika Kuposa Chuma”: (10 min.)
1 Tim. 6:6-8—Kufunika kokhala “wodzipereka kwa Mulungu ndi kukhala wokhutira ndi zimene tili nazo” (w03 6/1 9 ¶1-2)
1 Tim. 6:9—Mavuto amene anthu ofunitsitsa kulemera amakumana nawo (g 6/07 6 ¶2)
1 Tim. 6:10—Mavuto omwe amabwera chifukwa chokonda ndalama (g 11/08 6 ¶4-6)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
1 Tim. 4:2—Kodi munthu amaononga bwanji chikumbumtima chake, ndipo zimenezi ndi zoopsa bwanji? (lvs 23-24 ¶17)
1 Tim. 4:13—N’chifukwa chiyani Paulo analimbikitsa Timoteyo kuti azikhala wodzipereka pa nkhani yowerenga pamaso pa anthu? (it-2 714 ¶1-2)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 1 Tim. 4:1-16 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. Muitanireni kumisonkhano yathu. (th phunziro 11)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 4 min.) lvs 207-209 ¶20-21 (th phunziro 3)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) Sonyezani zimene mungachite mukamasiya kuphunzira Baibulo ndi munthu amene sakupita patsogolo.—Onani mwb19.02 7. (th phunziro 12)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Kukonda Chuma N’koopsa: (7 min.) Onerani vidiyo yakuti, Tiyenera ‘Kuthamanga Mopirira’—Tizipewa Zinthu Zosafunika Zomwe Zingangotitopetsa, kenako kambiranani zimene tikuphunzira.
“Kudzipereka kwa Mulungu N’kofunika Kuposa Kuchita Masewera”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Zimene Muyenera Kudziwa pa Nkhani Yochita Masewera.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 44
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 59 ndi Pemphero