Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 July tsamba 6
  • Kukhala Wodzipereka kwa Mulungu N’kofunika Kuposa Chuma

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kukhala Wodzipereka kwa Mulungu N’kofunika Kuposa Chuma
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Londolani Kudzipereka Kwaumulungu Monga Akristu Obatizidwa
    Nsanja ya Olonda​—1990
  • Tikulandirani ku Misonkhano Yachigawo ya “Kudzipereka Kwaumulungu”
    Nsanja ya Olonda—1989
  • Onjezerani Kudzipereka kwa Mulungu pa Chipiriro Chanu
    Nsanja ya Olonda—2002
  • Wonjezerani Pachipiriro Chanu Kudzipereka Kwaumulungu
    Nsanja ya Olonda—1993
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 July tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 TIMOTEYO 4-6

Kukhala Wodzipereka kwa Mulungu N’kofunika Kuposa Chuma

6:6-10

Kodi malemba otsatirawa akusonyeza bwanji kuti tingakhale osangalala kwambiri ngati titakhala wodzipereka kwa Mulungu m’malo mofunafuna chuma?

  • Mlongo anaika zithunzi pabolodi lomwe likusonyeza zinthu zosangalatsa zimene anapeza chifukwa chochita utumiki wa nthawi zonse

    Anthu amene akufuna kuyamba utumiki wa nthawi zonse adzapeza madalitso ambiri

    Mlal. 5:10

  • Mlal. 5:12

  • Mat. 5:3

  • Mac. 20:35

N’chifukwa chiyani n’zosatheka kukhala wodzipereka kwa Mulungu pa nthawi imodzimodziyo n’kumafunafuna chuma? (Mat. 6:24)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena