October 21-27
1 PETULO 3-5
Nyimbo Na. 14 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mapeto a Zinthu Zonse Ayandikira”: (10 min.)
1 Pet. 4:7—“Khalani oganiza bwino, ndipo khalani maso kuti musanyalanyaze kupemphera” (w13 11/15 3 ¶1)
1 Pet. 4:8—“Khalani okondana kwambiri” (w99 4/15 22 ¶3)
1 Pet. 4:9—“Muzicherezana popanda kudandaula” (w18.03 14-15 ¶2-3)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
1 Pet. 3:19, 20—Kodi ndi liti pamene Yesu “anapita kukalalikira kwa mizimu imene inali m’ndende” nanga anachita bwanji zimenezi? (w13 6/15 23)
1 Pet. 4:6—Kodi “uthenga wabwino unalengezedwa” kwa “akufa” ati? (w08 11/15 21 ¶8)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 1 Pet. 3:8-22 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 6)
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyi. (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Munthu Akhoza Kusintha Akaona Ulemu Komanso Khalidwe Lanu Labwino”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Yehova Amatilimbikitsa Kuti Tithe Kulimbana ndi Mavuto Athu.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 56
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero