Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 November tsamba 4
  • November 11-17

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 11-17
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 November tsamba 4

November 11-17

2 YOHANE 1-13; 3 YOHANE 1-14–YUDA 1-25

  • Nyimbo Na. 128 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tiyenera Kuchita Khama Kuti Tikhalebe m’Choonadi”: (10 min.)

    • [Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Yohane.]

    • [Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 3 Yohane.]

    • [Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yuda.]

    • Yuda 3​—Tiyenera “kumenya mwamphamvu nkhondo yachikhulupiriro” (w04 9/15 11-12 ¶8-9)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yuda 4, 12​—N’chifukwa chiyani anthu osaopa Mulungu omwe analowa mozemba mumpingo anayerekezeredwa ndi ‘miyala ikuluikulu yobisika m’madzi pa maphwando osonyezana chikondi’? (it-2 279, 816)

    • Yuda 14, 15​—N’chifukwa chiyani Inoki analankhula zam’tsogolo ngati kuti zachitika kale, nanga ulosi wakewu unakwaniritsidwa bwanji? (wp17.1 12 ¶1, 3)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 2 Yoh. 1-13 (th phunziro 12)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 6)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako musiyireni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 11)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 87

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 59

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 51 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena