Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 November tsamba 4
  • Tiyenera Kuchita Khama Kuti Tikhalebe m’Choonadi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tiyenera Kuchita Khama Kuti Tikhalebe m’Choonadi
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • “Mulimbanetu Chifukwa cha Chikhulupiriro”!
    Nsanja ya Olonda—1998
  • Chenjerani ndi Ampatuko!
    Nsanja ya Olonda—1991
  • Mfundo Zazikulu za M’makalata a Yohane ndi Yuda
    Nsanja ya Olonda—2008
  • Kulabadira Uthenga wa Yuda
    Imbirani Yehova Zitamando
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 November tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 2 YOHANE 1-13; 3 YOHANE 1-14–YUDA 1-25

Tiyenera Kuchita Khama Kuti Tikhalebe m’Choonadi

Yuda 3

Munthu akudzipanikiza pampata waung’ono wachitseko

Yesu anapereka malangizo akuti: “Yesetsani mwamphamvu kulowa pakhomo lopapatiza.” (Luka 13:24) Mawu a Yesuwa akusonyeza kuti munthu amafunika kuchita khama kuti akhale paubwenzi ndi Mulungu. Yuda, yemwe anali m’bale wake wa Yesu anauziridwa kulemba mfundo yofanana ndi imeneyi. Iye ananena kuti tiyenera “kumenya mwamphamvu nkhondo yachikhulupiriro.” Choncho m’pofunika khama kuti tizichita zotsatirazi:

  • Kupewa chiwerewere.​—Yuda 6, 7

  • Kulemekeza omwe ali ndi udindo.​—Yuda 8, 9

  • Kulimbitsa chikhulupiriro chathu “choyera kopambana,” pa zinthu zomwe timaphunzira.​—Yuda 20, 21

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena