Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 December tsamba 2
  • December 2-8

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 2-8
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 December tsamba 2

December 2-8

Chivumbulutso 7-9

  • Nyimbo Na. 63 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khamu Lalikulu la Anthu Likudalitsidwa ndi Yehova”: (10 min.)

    • Chiv. 7:9​—“Khamu lalikulu” linaimirira pamaso pa mpando wachifumu (it-1 997 ¶1)

    • Chiv. 7:14​—Khamu lalikulu lidzapulumuka “chisautso chachikulu” (it-2 1127 ¶4)

    • Chiv. 7:15-17​—Khamu lalikulu lidzakhala padziko lapansi ndipo lidzadalitsidwa kwambiri (it-1 996-997)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Chiv. 7:1​—Kodi ‘angelo anayi omwe anaimirira m’makona anayi a dziko lapansi’ komanso “mphepo zinayi” zikuimira chiyani? (re 115 ¶4)

    • Chiv. 9:11​—Kodi “mngelo wa phompho” ndi ndani? (it-1 12)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Chiv. 7:1-12 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kulankhula Mwachikondi Komanso Mokoma Mtima, kenako kambiranani phunziro 12 m’kabuku ka Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w16.01 25-26 ¶12-16​—Mutu: N’chifukwa Chiyani Sitiyenera Kuda Nkhawa ndi Kuwonjezereka kwa Anthu Odya Zizindikiro Komwe Kwachitika M’zaka Zapitazi? (th phunziro 6)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 93

  • Zofunika Pampingo: (8 min.)

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 62

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 31 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena