Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 December tsamba 6
  • December 30, 2019–January 5, 2020

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 30, 2019–January 5, 2020
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 December tsamba 6

December 30, 2019–January 5, 2020

CHIVUMBULUTSO 20-22

  • Nyimbo Na. 146 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano”: (10 min.)

    • Chiv. 21:1​—“Kumwamba kwakale ndi dziko lapansi lakale zinali zitachoka” (re 301 ¶2)

    • Chiv. 21:3, 4​—“Zakalezo zapita” (w13 12/1 11 ¶2-4)

    • Chiv. 21:5​—Malonjezo a Yehova ndi odalirika (w03 8/1 12 ¶14)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Chiv. 20:5​—Kodi “Akufa enawo” adzakhala bwanji ndi moyo kumapeto kwa zaka 1,000? (it-2 249 ¶2)

    • Chiv. 20:14, 15​—Kodi “Nyanja yamoto” ikuimira chiyani? (it-2 189-190)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Chiv. 20:1-15 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse. M’patseni kapepala komuitanira kumisonkhano yathu. (th phunziro 3)

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 4 min.) Sankhani lemba lililonse. M’patseni buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu. (th phunziro 9)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) jl phunziro 12 (th phunziro 6)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 57

  • “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Muzisintha Ulaliki Wanu”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 66

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 94 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena