Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 June tsamba 7
  • June 29–July 5

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 29–July 5
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 June tsamba 7

June 29–July 5

EKISODO 4-5

  • Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Ine Ndidzakhala Nawe Polankhula”: (10 min.)

    • Eks. 4:10, 13​—Mose ankadziona kuti sangakwanitse utumiki umene anapatsidwa (w10 10/15 13-14)

    • Eks. 4:11, 12​—Yehova anamutsimikizira kuti adzamuthandiza (w14 4/15 9 ¶5-6)

    • Eks. 4:14, 15​—Yehova anauza Mose kuti Aroni adzamuthandiza (w10 10/15 14)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Eks. 4:24-26​—N’chifukwa chiyani Zipora ananena kuti Yehova ndi “mkwati wa magazi”? (w04 3/15 28 ¶4)

    • Eks. 5:2​—Kodi Farao ankatanthauza chiyani ponena kuti sankamudziwa Yehova? (it-2 12 ¶5)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Eks. 4:1-17 (th phunziro 12)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako muitanireni kumisonkhano yathu. (th phunziro 2)

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu. (th phunziro 4)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) bhs 100 ¶15-16 (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 61

  • “Mmene Tingagwiritsire Ntchito Zitsanzo za Zimene Tinganene”: (5 min.) Nkhani yokambirana.

  • “Mungathe Kulalikira Komanso Kuphunzitsa”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzichita Zinthu Molimba Mtima​—Ofalitsa.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 89

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 118 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena