Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 June tsamba 6
  • “Ndidzakhala Amene Ndidzafune Kukhala”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Ndidzakhala Amene Ndidzafune Kukhala”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Kudziwa Dzina la Mulungu Kumatanthauza Chiyani?
    Nsanja ya Olonda—2010
  • Mwamuna ndi Mkazi Anapangidwa Kuti Azithandizana
    Nsanja ya Olonda—2007
  • “Taonani! Uyu Ndi Mulungu Wathu”
    Yandikirani Yehova
  • Akhristu Achinyamata, Kodi Mungatani Kuti Mukhale Olimba Mwauzimu?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 June tsamba 6
Mose wagwada pansi ndipo waphimba nkhope yake kuti asaone chitsamba chomwe chikuyaka moto.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 1-3

“Ndidzakhala Amene Ndidzafune Kukhala”

3:13, 14

Yehova anauza Mose chinthu chapadera kwambiri chokhudza iyeyo. Iye akhoza kukhala chilichonse chomwe chikufunikira kuti akwaniritse cholinga chake. Komabe sanyalanyaza mfundo zake zapamwamba akamachita zimenezi. Monga mmene makolo amasamalirira ana awo, Yehovanso amakhala chilichonse chomwe akufuna kuti asamalire ana ake.

Kodi Yehova anakhala bwanji chilichonse chomwe chinkafunika kuti andisamalire?

Zithunzi zosonyeza bambo akusamalira banja lake m’njira zosiyanasiyana. 1. Akuyankhula ndi mwana wake asanagone. 2. Akukambirana lemba la tsiku ndi mkazi wake komanso mwana wake. 3. Akuphunzitsa mwana wake kukwera njinga.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena