AUGUST 3-9
EKISODO 13-14
Nyimbo Na. 148 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Chilimikani ndi Kuona Chipulumutso cha Yehova”: (10 min.)
Eks 14:13, 14—Mose ankakhulupirira kuti Yehova apulumutsa Aisiraeli (w13 2/1 4)
Eks 14:21, 22—Yehova anawapulumutsa m’njira yodabwitsa kwambiri (w18.09 26 ¶13)
Eks 14:26-28—Yehova anawononga Farao ndi asilikali ake (w09 3/15 7 ¶2-3)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Eks 13:17—Kodi Yehova anasonyeza bwanji kuti ankaganizira Aisiraeli pamene ankawatulutsa mu Iguputo? (it-1 1117)
Eks 14:2—Kodi mwina ndi pati pamene Nyanja Yofiira inagawikana kuti Aisiraeli awoloke? (it-1 782 ¶2-3)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Eks 13:1-20 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Mawu Omaliza Abwino, kenako kambiranani phunziro 20 m’kabuku ka Kuphunzitsa.
Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w07 12/15 18-20 ¶13-16—Mutu: Kodi Tingaphunzire Chiyani pa Kupulumutsidwa kwa Aisiraeli pa Nyanja Yofiira? (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Limbani Mtima Pamene Mapeto Akuyandikira”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani mbali ina ya vidiyo yakuti, Kutsogoloku Tidzafunika Kulimba Mtima.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 94
Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)
Nyimbo Na. 47 ndi Pemphero