August Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Utumiki, August 2020. Zimene Tinganene August 3-9 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 13-14 “Chilimikani ndi Kuona Chipulumutso cha Yehova” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Limbani Mtima Pamene Mapeto Akuyandikira August 10-16 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 15-16 Tamandani Yehova Poimba Nyimbo MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzitamanda Yehova Pochita Upainiya August 17-23 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 17-18 Amuna Odzichepetsa Amaphunzitsa Ena N’kumawapatsa Zochita August 24-30 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 19-20 Mmene Malamulo 10 Amakukhudzirani August 31–September 6 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 21-22 Muzisonyeza Kuti Mumaona Moyo Mmene Yehova Amauonera