Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsamba 8
  • January 31–February 6

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 31–February 6
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 January tsamba 8

January 31–February 6

RUTE 3-4

  • Nyimbo Na. 39 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzikhala ndi Makhalidwe Abwino”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Ru 4:6​—Kodi munthu wowombola ‘akanawononga’ bwanji cholowa chake powombola mkazi? (w05 3/1 29 ¶3)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Ru 4:7-22 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • “Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki​—Muzithandiza Ophunzira Baibulo Anu Kuti Azipezeka Pamisonkhano”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzithandiza Amene Mukuphunzira Nawo Baibulo Kuti Azipezeka Pamisonkhano.

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 03 mfundo 4 (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 24

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 11 ndime 10-19, mawu akumapeto 26

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 124 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena