Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 2
  • May 1-7

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 1-7
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 2

May 1-7

2 MBIRI 17-19

  • Nyimbo Na. 114 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonera”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mb 17:9​—Kodi tingaphunzirepo chiyani pa ntchito yophunzitsa imene Yehosafati anayambitsa? (w17.03 20 ¶10-11)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 17:1-19 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya chitsanzo cha Ulendo Woyamba: Baibulo​—Aro 15:4. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 18)

  • Nkhani: (5 min.) w21.05 17-18 ¶11-15​—Mutu: Tizisangalalabe Ngakhale Pamene Anthu Sakufuna Kumvetsera. (th phunziro 16)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 104

  • “Muzidziona Mmene Yehova Amakuonerani”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 44 mfundo 5-6, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 111 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena