May Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu, May-June 2023 May 1-7 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonera MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzidziona Mmene Yehova Amakuonerani May 8-14 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mwakonzeka Kukumana ndi Mavuto Azachuma? May 15-21 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Amadalitsa Anthu Amene Amachita Zinthu Molimba Mtima May 22-28 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Yehova Akhoza Kukupatsani Zambiri Kuposa Pamenepa” May 29–June 4 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mukhoza Kutumikira Yehova Ngakhale Makolo Anu Si Chitsanzo Chabwino MOYO WATHU WACHIKHRISTU Yehova ndi “Tate wa Ana Amasiye” June 5-11 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kusonkhana Pamodzi Kumatithandiza June 12-18 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzilimbikitsa Abale ndi Alongo Anu Akakumana ndi Mavuto MOYO WATHU WACHIKHRISTU Dzitetezeni kwa Anthu Ampatuko June 19-25 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Mawu a Mulungu Amakuthandizani Mokwanira? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mukugwiritsa Ntchito Mokwanira Baibulo Longomvetsera? June 26–July 2 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzilola Kuti Yehova Azikugwiritsani Ntchito MOYO WATHU WACHIKHRISTU Mumasangalala Mukamayambitsa Nkhani KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Zimene Tinganene