Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 15
  • Mumasangalala Mukamayambitsa Nkhani

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mumasangalala Mukamayambitsa Nkhani
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Zosankha Zomwe Zimasonyeza Kuti Timadalira Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Zimene Inuyo Mwachita
    Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso
  • Tizivomereza Modzichepetsa Kuti Sitikudziwa Zonse
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2025
  • Muziwerenga Baibulo Tsiku Lililonse Komanso Muzifunafuna Nzeru
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 15

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Mumasangalala Mukamayambitsa Nkhani

Kucheza ndi imodzi mwa njira zosangalatsa komanso zothandiza kwambiri zomwe tingagwiritse ntchito kuti tilalikire. Komabe, tikhoza kuchita mantha kuti tiyambitse nkhani ngati timangoganizira kwambiri za mmene tingayambire kukambirana nkhani ya m’Baibulo. M’malo momaganizira kwambiri za mmene mungalalikirire, muzimusonyeza chidwi munthuyo. (Mt 22:39; Afi 2:4) Ngati pamene mukucheza mwayi wapezeka woti mufotokoze za chikhulupiriro chanu, pali zinthu zambiri zomwe zingakuthandizeni.

Kodi zinthu zotsatirazi zingakuthandizeni bwanji kulalikira zokhudza nkhani imene yangobwera pamene mukucheza?

Makadi odziwitsa anthu za JW.ORG.
Chizindikiro cha jw.org.
Zithunzi zosonyeza timapepala tosiyanasiyana: 1. “Kodi Baibulo Mumalikhulupirira?” 2. “Kodi Mukuganiza Kuti Zinthu Zidzakhala Bwanji M’tsogolo?” 3. “Kodi N’chiyani Chingathandize Kuti Banja Likhale Losangalala?” 4. “Kodi Dziko Lapansi Lili M’manja mwa Ndani?” 5. “Kodi Mavuto Amene Tikukumana Nawowa Adzathadi?” 6. “Kodi N’zoonadi Kuti Akufa Adzauka?” 7. “Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani?” 8. “Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?”

ONERANI VIDIYO YAKUTI “CHITSULO CHIMANOLA CHITSULO CHINZAKE”​—MMENE MUNGAYAMBIRE KUCHEZA NDI ANTHU, KENAKO YANKHANI FUNSO LOTSATIRALI:

Kodi ndi mfundo zitatu ziti zimene zingatithandize kuwonjezera luso lathu loyamba kucheza ndi anthu?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena