Mupeze Mayankho a Mafunso Awa:
1. Kodi tingamve bwanji “zimene mzimu ukunena”? (Chiv. 1:3, 10, 11; 3:19)
2. Kodi n’chiyani chingatithandize kuti tipitirizebe kuchita khama komanso kupirira? (Chiv. 2:4)
3. Kodi tingakonzekere bwanji kuti tidzathe kupirira molimba mtima tikamadzazunzidwa? (Miy. 29:25; Chiv. 2:10, 11)
4. Kodi tingatani kuti tisakane kuti timakhulupirira Yesu? (Chiv. 2:12-16)
5. Kodi tingatani kuti tipitirize kugwira mwamphamvu chimene tili nacho? (Chiv. 2:24, 25; 3:1-3, 7, 8, 10, 11)
6. Kodi n’chiyani chingatithandize kukhalabe odzipereka? (Chiv. 3:14-19; Mat. 6:25-27, 31-33)
© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
CA-brpgm26-CN