Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsamba 15
  • Zosankha Zomwe Zimasonyeza Kuti Timadalira Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zosankha Zomwe Zimasonyeza Kuti Timadalira Yehova
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
    Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woyang’anira Dera wa 2025-2026
  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
    Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woimira Nthambi wa 2025-202
  • Muziwerenga Baibulo Tsiku Lililonse Komanso Muzifunafuna Nzeru
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Zimene Inuyo Mwachita
    Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 March tsamba 15

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Zosankha Zomwe Zimasonyeza Kuti Timadalira Yehova

Tsiku lililonse, timafunika kusankha zinthu zosiyanasiyana. Nthawi zambiri anthu m’dzikoli amasankha zinthu potengera mmene akumvera mumtima kapena amangotsanzira zimene anthu ambiri amachita. (Eks 23:2; Miy 28:26) Koma mosiyana ndi zimenezi, anthu amene amadalira Yehova ‘amamukumbukira’ mwa kugwiritsa ntchito mfundo za m’Baibulo kuti ziziwatsogolera akamasankha zochita.​—Miy 3:5, 6.

Pa lemba lililonse m’munsimu, lembani nkhani yosonyeza mmene lembalo lingakuthandizireni posankha zinthu mwanzeru.

  • Mt 6:33

  • Aro 12:18

  • 1Ak 10:24

  • Aef 5:15, 16

  • 1Ti 2:9, 10

  • Ahe 13:5

ONERANI VIDIYO YAKUTI MUZITSANZIRA ANTHU A CHIKHULUPIRIRO, OSATI OPANDA CHIKHULUPIRIRO​—MOSE, OSATI FARAO, KENAKO YANKHANI FUNSO LOTSATIRALI:

Chithunzi cha muvidiyo yakuti “Muzitsanzira Anthu A Chikhulupiriro, Osati Opanda Chikhulupiriro​—Mose, Osati Farao.” M’bale akupita kumsonkhano ndipo walandira foni yadzidzidzi kuchokera kuntchito.

Kodi chitsanzo cha m’Baibulo chinathandiza bwanji m’bale wa muvidiyoyi kuti asankhe zinthu moyenera?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena