Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsamba 11
  • Muziwerenga Baibulo Tsiku Lililonse Komanso Muzifunafuna Nzeru

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muziwerenga Baibulo Tsiku Lililonse Komanso Muzifunafuna Nzeru
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Zosankha Zomwe Zimasonyeza Kuti Timadalira Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Zimene Inuyo Mwachita
    Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso
  • Tizivomereza Modzichepetsa Kuti Sitikudziwa Zonse
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2025
  • Zimene Tingachite Kuti Tizisangalala Kwambiri Tikamalalikira
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 March tsamba 11

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muziwerenga Baibulo Tsiku Lililonse Komanso Muzifunafuna Nzeru

Nzeru zochokera kwa Mulungu ndi zamtengo wapatali mofanana ndi chuma chobisika. (Miy 2:1-6) Nzeru zimatithandiza kuti tiziganiza bwino, tizisankha bwino zochita komanso zimatiteteza. Choncho “nzeru ndiyo chinthu chofunika kwambiri.” (Miy 4:5-7) Pamafunika khama kuti tifufuze chuma chauzimu chobisika cha m’Mawu a Mulungu. Tikhoza kuyamba ndi kuwerenga Mawu a Mulungu “usana ndi usiku,” kapena kuti tsiku lililonse. (Yos 1:8) Onani mfundo zimene zingatithandize kuti tiziwerenga komanso kusangalala ndi Mawu a Mulungu tsiku ndi tsiku.

ONERANI VIDIYO YAKUTI ACHINYAMATA AKUPHUNZIRA KUKONDA MAWU A MULUNGU, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

Kodi achinyamatawa anakumana ndi mavuto otani pamene ankafuna kuti aziwerenga Baibulo tsiku lililonse, nanga n’chiyani chimene chinawathandiza?

  • Zithunzi za muvidiyo yakuti “Achinyamata Akuphunzira Kukonda Mawu a Mulungu.” Melanie.

    Melanie

  • Zithunzi za muvidiyo yakuti “Achinyamata Akuphunzira Kukonda Mawu a Mulungu.” Samuel.

    Samuel

  • Zithunzi za muvidiyo yakuti “Achinyamata Akuphunzira Kukonda Mawu a Mulungu.” Celine.

    Celine

  • Zithunzi za muvidiyo yakuti “Achinyamata Akuphunzira Kukonda Mawu a Mulungu.” Raphaello.

    Raphaello

NDANDANDA YANGA YOWERENGERA BAIBULO:

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena