Mupeze Mayankho a Mafunso Awa:
1. Kodi Yehova akufuna anthu otani? (Yoh. 4:23, 24)
2. Kodi mzimu woyera umatithandiza bwanji kuti tizim’patsa Yehova zonse zomwe tingathe? (Mac. 16:6-10; 1 Akor. 2:10-13; Afil. 4:8, 9)
3. Kodi ‘timachititsa bwanji choonadi kuti chidziwike’? (2 Akor. 4:1, 2)
4. Kodi kulambira motsogoleredwa ndi choonadi kumaphatikizapo chiyani? (Miy. 24:3; Yoh. 18:36, 37; Aef. 5:33; Aheb. 13:5, 6, 18)
5. Kodi tingatani kuti ‘tigule choonadi ndipo tisachigulitse’? (Miy. 23:23)
© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
CA-copgm26-CN